Malawi
Mwachidule
Select inayamba kugwira ntchito muno M’Malawi kumapeto a chaka cha 2009 ndipo ngongole yoyamba inaperekedwa mu February 2011. Mu August mchaka cha 2010, Select Malawi inalowa mumgwirizano ndi a Soros Economic Development Fund omwe anali okonzeka kupereka chithandizo kwa mabungwe omwe amafuna kupereka ngongole zokhudzana ndi zomanga nyumba mdziko la Malawi lomwe ndi losauka. Ndipo ngongole ya Select yochokera ku Soros Economic Development Fund inaperekedwa kudzera mundondomeko wazachuma pogwiritsa nthchito bank ya First Merchant (FMB).
Pozindikira kuti maunduna ambiri likulu lawo liri ku Lilongwe, Select inaganiza zokhanzikitsa ofesi yake yayikulu mumzindawu kuti izitha kulumikizana bwino ndi akulu akulu aboma. Select ili ndi ofesi zina mumzida wa Blantyre ndi Mzuzu komanso ofesi zazing’ono zokwana 19 madela ambiri muno mMalawi.
Select Financial Services panopa ndilimodzi la mabungwe akuluakulu omwe ndi akatswiri mu gawo lopereka ngongole zingongono kwa a Amalawi komanso ndilokhalo lomwe likupereka ngongole zokhudzana ndi zomanga nyumba.
Mawelengero a ngongole
Mungatipeze bwanji

Mkulu wa kampani: James Kajamu
Malo omwe tikupezeka:
Ofesi ya Lilongwe
Shop 7 ndi 8,
Hayyat Complex,
Kamuzu Procession Way,
P O Box 2489,
Lilongwe,
Malawi
Lamya: +265 175 8861
Fax Number: +265 175 8866
Nthambi yaku Blantyre
Bwana Wamkulu wa Ofesi:Harriet Saukira
Malo omwe tikupezeka:
Appollo Arcade,
Livingstone Avenue,
Blantyre
Bokosi:
C/O African Alliance
P.O BOX 3340
Blantyre
Lamya:
+265 18 30780 | +265 18 32356
Nthambii ya Mzuzu
Bwana Wamkulu wa ofesi: Paul Kavuta
Malo omwe mungatipeze:
Lutho Arcade, Moyanganizana ndi Malawi Revenue Authority (MRA)
Bokosi:
C/O Lutho Arcade
P.O.Box 225
Mzuzu
Gulu lotsogolera







