Malawi
Ku Select bizinesi ikupitilira!
Nthawi yogwirira ntchito munyengo ino ya corona kapena COVID-19: Lolemba mpaka lachisanu: 8 koloko m’mawa mpakana 5 koloko madzulo, Loweluka: 8 koloko m’mawa mpakana 12 koloko masana
Koma kugwa kwa mlili wa Civid-19, tachepetsa kukumana ndi makasitomala (kupewa kupotsa kuchiza).
Ogwila ntchito athu ali okonzeka kunva kuchokera kwa inu makasitomala athu kudzera pa ma telefoni nambala awa, komanso kudzera njira a imelo izi:
Mafunso osiyanasiyana:
Gift Mpoola:
+265 8873 86343 | mpoolam@selectafrica.net
Queen Phiri:
+265 8873 86345 | phiriq@selectafrica.net
Madalitso Goneka:
+265 8873 86344 | gonekam@selectafrica.net
Zolipira kapena kubweza ngongole:
McWilly Toto:
+265 8883 80273 | mcwillym@selectafrica.net
Estery Simtowe:
+265 9994 85323 | simtowee@selectafrica.net
Othandizira kuyankha za pa ofesi:
Christine Banda:
+265 9992 76117 | bandac@selectafrica.net
Mwachidule
Select inayamba kugwira ntchito muno M’Malawi kumapeto a chaka cha 2009 ndipo ngongole yoyamba inaperekedwa mu February 2011. Mu August mchaka cha 2010, Select Malawi inalowa mumgwirizano ndi a Soros Economic Development Fund omwe anali okonzeka kupereka chithandizo kwa mabungwe omwe amafuna kupereka ngongole zokhudzana ndi zomanga nyumba mdziko la Malawi lomwe ndi losauka. Ndipo ngongole ya Select yochokera ku Soros Economic Development Fund inaperekedwa kudzera mundondomeko wazachuma pogwiritsa nthchito bank ya First Merchant (FMB).
Pozindikira kuti maunduna ambiri likulu lawo liri ku Lilongwe, Select inaganiza zokhanzikitsa ofesi yake yayikulu mumzindawu kuti izitha kulumikizana bwino ndi akulu akulu aboma. Select ili ndi ofesi zina mumzida wa Blantyre ndi Mzuzu komanso ofesi zazing’ono zokwana 19 madela ambiri muno mMalawi.
Select Financial Services panopa ndilimodzi la mabungwe akuluakulu omwe ndi akatswiri mu gawo lopereka ngongole zingongono kwa a Amalawi komanso ndilokhalo lomwe likupereka ngongole zokhudzana ndi zomanga nyumba.
Mawelengero a ngongole
MUNGATIPEZE BWANJI
Malo omwe tikupezeka: Bokosi: Lamya: +265 1 774 680/6/7 | Nthambi yaku Blantyre Bwana Wamkulu wa Ofesi: Madalitso Goneka Malo omwe tikupezeka: Bokosi: Lamya: | |
Nthambii ya Mzuzu Bwana Wamkulu wa ofesi: Gift Mpoola Malo omwe mungatipeze: Bokosi: Lamya: |
GULU LOTSOGOLERA
CEO Webster Mbekeani | Deputy CEO/COO Vacant | GIFT CHIBWANA Chief Financial Officer | ZEENAT OSMAN Compliance Manager |
BONIFACE MATEKENYA Compliance Manager | GIFT MPOOLA Regional Manager (North) | MADALITSO GONEKA Regional Manager (South) | EDWIN MAGOLA Regional Manager (Centre) magolae@selectafrica.net |